Yeremiya 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Bwererani, inu ana opanduka.+ Ndidzachiritsa kusakhulupirika kwanu.”+ “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu, pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+ Yeremiya 50:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “M’masiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo+ ana a Isiraeli pamodzi ndi ana a Yuda adzabwera,”+ watero Yehova. “Iwo adzayenda akulira+ ndipo adzafunafuna Yehova Mulungu wawo.+
22 “Bwererani, inu ana opanduka.+ Ndidzachiritsa kusakhulupirika kwanu.”+ “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu, pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+
4 “M’masiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo+ ana a Isiraeli pamodzi ndi ana a Yuda adzabwera,”+ watero Yehova. “Iwo adzayenda akulira+ ndipo adzafunafuna Yehova Mulungu wawo.+