Hoseya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ana a Isiraeli adzabwerera ndi kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndiponso Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera+ ndipo adzafunafuna ubwino wake m’masiku otsiriza.+ Zekariya 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu okhala mumzinda umodzi adzapita kwa anthu okhala mumzinda wina n’kuwauza kuti: “Tiyeni tipite!+ Tiyeni tipite kukakhazika pansi mtima+ wa Yehova ndi kufunafuna Yehova wa makamu. Inenso ndipita nawo.”+
5 Kenako ana a Isiraeli adzabwerera ndi kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndiponso Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera+ ndipo adzafunafuna ubwino wake m’masiku otsiriza.+
21 Anthu okhala mumzinda umodzi adzapita kwa anthu okhala mumzinda wina n’kuwauza kuti: “Tiyeni tipite!+ Tiyeni tipite kukakhazika pansi mtima+ wa Yehova ndi kufunafuna Yehova wa makamu. Inenso ndipita nawo.”+