Ezekieli 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘“Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo.+ Onse adzakhala ndi m’busa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga+ ndipo adzasunga malamulo anga+ ndi kuwatsatira.+ Luka 1:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Iye watikwezera ife nyanga*+ yachipulumutso m’nyumba ya mtumiki wake Davide, Machitidwe 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye anali mneneri, ndipo anali kudziwa kuti Mulungu anam’lonjeza mwa lumbiro, kuti pampando wake wachifumu adzakhazikapo mmodzi mwa zipatso za m’chiuno mwake.+ Machitidwe 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kuchokera mwa ana+ a munthu ameneyu, malinga ndi lonjezo lake, Mulungu wabweretsa mpulumutsi mu Isiraeli,+ amene ndi Yesu.
24 “‘“Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo.+ Onse adzakhala ndi m’busa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga+ ndipo adzasunga malamulo anga+ ndi kuwatsatira.+
30 Iye anali mneneri, ndipo anali kudziwa kuti Mulungu anam’lonjeza mwa lumbiro, kuti pampando wake wachifumu adzakhazikapo mmodzi mwa zipatso za m’chiuno mwake.+
23 Kuchokera mwa ana+ a munthu ameneyu, malinga ndi lonjezo lake, Mulungu wabweretsa mpulumutsi mu Isiraeli,+ amene ndi Yesu.