Salimo 91:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+ Salimo 121:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova akukuyang’anira.+Yehova ndiye mthunzi wako+ kudzanja lako lamanja.+ Salimo 121:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Masana dzuwa silidzakupweteka,+Kapenanso mwezi usiku.+ Chivumbulutso 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo sadzamvanso njala kapena ludzu. Dzuwa kapena kutentha kulikonse sikudzawawotcha,+
91 Aliyense wokhala m’malo otetezeka+ a Wam’mwambamwamba+Adzakhala wosungika mumthunzi wa Wamphamvuyonse.+