Salimo 121:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Masana dzuwa silidzakupweteka,+Kapenanso mwezi usiku.+ Yesaya 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sadzakhala ndi njala+ ndipo sadzamva ludzu.+ Sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Pakuti yemwe amawamvera chisoni adzawatsogolera+ ndipo adzapita nawo ku akasupe amadzi.+
10 Iwo sadzakhala ndi njala+ ndipo sadzamva ludzu.+ Sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Pakuti yemwe amawamvera chisoni adzawatsogolera+ ndipo adzapita nawo ku akasupe amadzi.+