Yesaya 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye.+ Inde bwerani mudzagule vinyo+ ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo wake.+
55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye.+ Inde bwerani mudzagule vinyo+ ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo wake.+