Yesaya 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye. Inde bwerani mudzagule vinyo ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2018, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,3/15/2002, tsa. 8 Yesaya 2, ptsa. 233-235, 241
55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye. Inde bwerani mudzagule vinyo ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo.+
55:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2018, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,3/15/2002, tsa. 8 Yesaya 2, ptsa. 233-235, 241