Chivumbulutso 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anandiuza kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega,* chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense amene akumva ludzu ndidzamupatsa madzi a kasupe wa moyo kwaulere.*+ Chivumbulutso 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mzimu ndi mkwatibwi+ akupitiriza kunena kuti, “Bwera!” ndipo aliyense amene wamva anene kuti, “Bwera!” Komanso aliyense amene akumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi opatsa moyo kwaulere.+
6 Iye anandiuza kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega,* chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense amene akumva ludzu ndidzamupatsa madzi a kasupe wa moyo kwaulere.*+
17 Mzimu ndi mkwatibwi+ akupitiriza kunena kuti, “Bwera!” ndipo aliyense amene wamva anene kuti, “Bwera!” Komanso aliyense amene akumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi opatsa moyo kwaulere.+