Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 36:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Inu ndinu kasupe wa moyo.+

      Chifukwa cha kuwala kochokera kwa inu, timaona kuwala.+

  • Yesaya 55:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+

      Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye.

      Inde bwerani mudzagule vinyo ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo.+

  • Chivumbulutso 7:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa Mwanawankhosa,+ amene ali pambali* pa mpando wachifumu, adzawaweta+ nʼkuwatsogolera ku akasupe a madzi a moyo.+ Ndipo Mulungu adzapukuta misozi yonse mʼmaso mwawo.”+

  • Chivumbulutso 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo,+ oyera ngati mwala wonyezimira wa kulusitalo, ukuyenda kuchokera kumpando wachifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawankhosa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena