Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 42:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mofanana ndi munthu amene akulakalaka madzi, ndikulakalaka* Mulungu, Mulungu wamoyo.+

      Ndidzapita liti kukaonekera pamaso pa Mulungu?*+

  • Salimo 63:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+

      Ine ndikulakalaka inu.*+

      Ndalefuka* chifukwa cholakalaka inu

      Mʼdziko louma komanso lopanda madzi, kumene sikumera chilichonse.+

  • Amosi 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubwera

      Pamene ndidzatumiza njala mʼdziko.

      Osati njala ya chakudya kapena ludzu lofuna madzi,

      Koma njala yofuna kumva mawu a Yehova.+

  • Mateyu 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Osangalala ndi anthu amene akumva njala ndi ludzu+ la chilungamo chifukwa adzakhuta.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena