Salimo 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Moyo wanga ukulakalaka Mulungu,+ ukulakalaka Mulungu wamoyo.+Ndidzapita liti kunyumba ya Mulungu kukaonekera pamaso pake?+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:2 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 91/15/1995, tsa. 19
2 Moyo wanga ukulakalaka Mulungu,+ ukulakalaka Mulungu wamoyo.+Ndidzapita liti kunyumba ya Mulungu kukaonekera pamaso pake?+