Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 42:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Moyo wanga ukulakalaka Mulungu,+ ukulakalaka Mulungu wamoyo.+

      Ndidzapita liti kunyumba ya Mulungu kukaonekera pamaso pake?+

  • Salimo 63:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+

      Moyo wanga ukulakalaka inu.+

      Thupi langa lalefuka chifukwa cholakalaka inu

      M’dziko louma ndi lopanda chonde, lopanda madzi.+

  • Amosi 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Taonani, masiku akubwera pamene ndidzatumiza njala m’dziko. Njala imeneyo siidzakhala ya chakudya kapenanso ludzu lofuna madzi ayi, koma idzakhala njala ndiponso ludzu lofuna kumva mawu a Yehova.+

  • Mateyu 5:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Odala ndi anthu amene akumva njala ndi ludzu+ la chilungamo, chifukwa adzakhuta.+

  • Chivumbulutso 21:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anandiuzanso kuti: “Zakwaniritsidwa! Ine ndine Alefa ndi Omega, chiyambi ndi mapeto.+ Aliyense womva ludzu, ndidzamupatsa madzi a m’kasupe wa moyo kwaulere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena