Yesaya 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye.+ Inde bwerani mudzagule vinyo+ ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo wake.+ Luka 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Inu amene mukumva njala+ tsopano ndinu odala, chifukwa mudzakhuta.+ “Inu amene mukulira tsopano ndinu odala, chifukwa mudzaseka.+
55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye.+ Inde bwerani mudzagule vinyo+ ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo wake.+
21 “Inu amene mukumva njala+ tsopano ndinu odala, chifukwa mudzakhuta.+ “Inu amene mukulira tsopano ndinu odala, chifukwa mudzaseka.+