Yoweli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+ 1 Akorinto 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinakupatsani mkaka, osati chakudya chotafuna,+ chifukwa munali musanalimbe mokwanira. Komatu ngakhale tsopano simunalimbebe mokwanira,+ 1 Petulo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma monga makanda obadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasukuluka+ umene uli m’mawu a Mulungu, kuti mwa kumwa mkakawo, mukule ndi kukhala oyenera chipulumutso,+
18 “Nthawi imeneyo mapiri adzachucha vinyo wotsekemera.+ Mkaka udzayenda pazitunda ndipo m’mitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe wamadzi adzatuluka m’nyumba ya Yehova+ ndi kuthirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.+
2 Ndinakupatsani mkaka, osati chakudya chotafuna,+ chifukwa munali musanalimbe mokwanira. Komatu ngakhale tsopano simunalimbebe mokwanira,+
2 Koma monga makanda obadwa kumene,+ muzilakalaka mkaka wosasukuluka+ umene uli m’mawu a Mulungu, kuti mwa kumwa mkakawo, mukule ndi kukhala oyenera chipulumutso,+