Salimo 107:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wapereka madzi kwa anthu aludzu.+Ndipo anthu anjala wawadyetsa zinthu zabwino.+ Yeremiya 31:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti ndidzatsitsimutsa wolefuka ndipo ndidzalimbitsa wofooka aliyense.”+