Aroma 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiponso, kuyesedwa olungama chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene wakusonyeza, powamasula ndi dipo+ lolipiridwa ndi Khristu Yesu, kuli ngati mphatso yaulere.+ 1 Akorinto 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho mphoto yanga ndi chiyani? Ndi yakuti polengeza uthenga wabwino ndipereke uthengawo kwaulere,+ kuti ndisagwiritse ntchito molakwa ufulu wanga pa zinthu zokhudzana ndi uthenga wabwino. Chivumbulutso 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mzimu+ ndi mkwatibwi+ akunenabe kuti: “Bwera!” Aliyense wakumva anene kuti: “Bwera!”+ Aliyense wakumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi a moyo kwaulere.+
24 Ndiponso, kuyesedwa olungama chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene wakusonyeza, powamasula ndi dipo+ lolipiridwa ndi Khristu Yesu, kuli ngati mphatso yaulere.+
18 Choncho mphoto yanga ndi chiyani? Ndi yakuti polengeza uthenga wabwino ndipereke uthengawo kwaulere,+ kuti ndisagwiritse ntchito molakwa ufulu wanga pa zinthu zokhudzana ndi uthenga wabwino.
17 Mzimu+ ndi mkwatibwi+ akunenabe kuti: “Bwera!” Aliyense wakumva anene kuti: “Bwera!”+ Aliyense wakumva ludzu abwere.+ Aliyense amene akufuna, amwe madzi a moyo kwaulere.+