17 Ngati chifukwa cha uchimo wa munthu mmodziyo+ imfa inalamulira monga mfumu+ kudzera mwa munthuyo, amene alandira kukoma mtima kwakukulu+ kochuluka ndiponso mphatso yaulere+ yaikuluyo ya chilungamo, adzakhala ndi moyo ndi kulamulira monga mafumu+ kudzera mwa munthu mmodziyu, Yesu Khristu.+