1 Petulo 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pajatu ngakhale Khristu anafera machimo kamodzi kokha basi.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama,+ kuti akufikitseni kwa Mulungu.+ Iye anaphedwa m’thupi,+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+ Chivumbulutso 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “Woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,”+ ndiponso “Wolamulira wa mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda,+ amenenso anatimasula ku machimo athu ndi magazi ake enieniwo,+
18 Pajatu ngakhale Khristu anafera machimo kamodzi kokha basi.+ Munthu wolungamayo anafera anthu osalungama,+ kuti akufikitseni kwa Mulungu.+ Iye anaphedwa m’thupi,+ koma anaukitsidwa monga mzimu.+
5 Komanso, kuchokera kwa Yesu Khristu, “Mboni Yokhulupirika,”+ “Woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,”+ ndiponso “Wolamulira wa mafumu a dziko lapansi.”+ Kwa iye amene amatikonda,+ amenenso anatimasula ku machimo athu ndi magazi ake enieniwo,+