Ekisodo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+ Numeri 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye sanaone mphamvu yamatsenga+ iliyonse ikuchita kanthu pa Yakobo,Ndipo sanaone Isiraeli akuponyeredwa vuto.Mulungu wake Yehova ali naye,+Ndipo mfuu yotamanda mfumu ikumveka pakati pake.
2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+
21 Iye sanaone mphamvu yamatsenga+ iliyonse ikuchita kanthu pa Yakobo,Ndipo sanaone Isiraeli akuponyeredwa vuto.Mulungu wake Yehova ali naye,+Ndipo mfuu yotamanda mfumu ikumveka pakati pake.