Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 22:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Yehova ndi wamoyo.+ Lidalitsike Thanthwe langa.+

      Mulungu wanga, thanthwe limene limandipulumutsa likhale lokwezeka.+

  • Salimo 99:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kwezani Yehova Mulungu wathu+ ndipo muweramireni pachopondapo mapazi ake.+

      Iye ndi woyera.+

  • Yesaya 25:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Inu Yehova, ndinu Mulungu wanga.+ Ndikukukwezani+ ndi kutamanda dzina lanu+ chifukwa mwachita zinthu zabwino kwambiri.+ Mwakwaniritsa zolinga zanu+ zakalekale ndipo mwachita zinthu mokhulupirika+ ndi modalirika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena