Salimo 99:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kwezani Yehova Mulungu wathu+ ndipo mugwadireni* pachopondapo mapazi ake.+Iye ndi woyera.+