Ekisodo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndipo anati: “Popeza dzanja laukira mpando wachifumu+ wa Ya,+ Yehova adzamenya nkhondo ndi Aamaleki ku mibadwomibadwo.”+ Salimo 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzakukondani inu Yehova, mphamvu yanga.+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+
16 ndipo anati: “Popeza dzanja laukira mpando wachifumu+ wa Ya,+ Yehova adzamenya nkhondo ndi Aamaleki ku mibadwomibadwo.”+
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+