Numeri 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye sangalole kuti mphamvu zilizonse zamatsenga zivulaze Yakobo,Ndipo sangalole kuti Isiraeli akumane ndi vuto lililonse. Mulungu wake Yehova ali naye,+Ndipo amamutamanda mofuula monga mfumu yawo.
21 Iye sangalole kuti mphamvu zilizonse zamatsenga zivulaze Yakobo,Ndipo sangalole kuti Isiraeli akumane ndi vuto lililonse. Mulungu wake Yehova ali naye,+Ndipo amamutamanda mofuula monga mfumu yawo.