Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 22:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 “Ukabwereketsa ndalama kwa anthu anga, kwa munthu wovutika amene ali pafupi ndi iwe,+ usakhale ngati munthu wopereka ngongole yakatapira* kwa iye. Usafunepo chiwongoladzanja.+

  • Levitiko 25:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Musamalandire chiwongoladzanja kwa iye kapena kumukongoza mwa katapira,*+ koma muziopa Mulungu wanu.+ Mnansi wanu ayenera kukhala ndi moyo pakati panu.

  • Deuteronomo 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “M’bale wako usamulipiritse chiwongoladzanja+ pa ndalama, chakudya+ kapena chilichonse chimene munthu angafunepo chiwongoladzanja.

  • Ezekieli 18:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iye sapondereza munthu wosautsika. Sakongoza zinthu mwa katapira+ ndipo salandira chiwongoladzanja.+ Amatsatira zigamulo zanga+ ndi kuyenda motsatira malamulo anga.+ Munthu wotere sadzafa chifukwa cha zolakwa za bambo ake.+ Adzakhalabe ndi moyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena