Ezekieli 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ngati akuyendabe m’malamulo anga+ ndi kusunga zigamulo zanga kuti azichita mogwirizana ndi choonadi,+ ndiye kuti munthu wotero ndi wolungama.+ Ndithu adzakhalabe ndi moyo,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
9 ngati akuyendabe m’malamulo anga+ ndi kusunga zigamulo zanga kuti azichita mogwirizana ndi choonadi,+ ndiye kuti munthu wotero ndi wolungama.+ Ndithu adzakhalabe ndi moyo,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.