Levitiko 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo.+ Musamachite chinyengo poyeza utali wa chinthu, kulemera kwa chinthu+ kapena poyeza zinthu zamadzi. Deuteronomo 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti aliyense wochita zimenezi, aliyense wosachita chilungamo, n’ngonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+
35 “‘Musamaweruze mopanda chilungamo.+ Musamachite chinyengo poyeza utali wa chinthu, kulemera kwa chinthu+ kapena poyeza zinthu zamadzi.
16 Pakuti aliyense wochita zimenezi, aliyense wosachita chilungamo, n’ngonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+