Deuteronomo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “M’thumba lako, usakhale ndi miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu,+ usakhale ndi muyezo waukulu ndi wina waung’ono. Deuteronomo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muyezo wako woyezera kulemera kwa chinthu uzikhala wolondola ndi woyenera. Muyezo wako wa efa uzikhala wolondola ndi woyenera kuti masiku ako achuluke m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Miyambo 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu ndiponso miyezo iwiri yosiyana ya efa,*+ zonsezi n’zonyansa kwa Yehova.+
13 “M’thumba lako, usakhale ndi miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu,+ usakhale ndi muyezo waukulu ndi wina waung’ono.
15 Muyezo wako woyezera kulemera kwa chinthu uzikhala wolondola ndi woyenera. Muyezo wako wa efa uzikhala wolondola ndi woyenera kuti masiku ako achuluke m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+
10 Miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu ndiponso miyezo iwiri yosiyana ya efa,*+ zonsezi n’zonyansa kwa Yehova.+