Levitiko 25:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Musamalandire chiwongoladzanja kwa iye kapena kumukongoza mwa katapira,*+ koma muziopa Mulungu wanu.+ Mnansi wanu ayenera kukhala ndi moyo pakati panu. Ezekieli 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu alandira ziphuphu kuti akhetse magazi.+ Iwe walandira chiwongoladzanja+ ndi kuchita katapira.+ Ukupeza phindu losayenera mwa kubera anzako+ mwachinyengo+ ndipo ine wandiiwala,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
36 Musamalandire chiwongoladzanja kwa iye kapena kumukongoza mwa katapira,*+ koma muziopa Mulungu wanu.+ Mnansi wanu ayenera kukhala ndi moyo pakati panu.
12 Anthu alandira ziphuphu kuti akhetse magazi.+ Iwe walandira chiwongoladzanja+ ndi kuchita katapira.+ Ukupeza phindu losayenera mwa kubera anzako+ mwachinyengo+ ndipo ine wandiiwala,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.