Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 18:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Izi n’zimene zimachitikira malo okhala munthu woipa,

      Ndipo awa ndiwo malo a munthu wosadziwa Mulungu.”

  • 1 Atesalonika 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 osati mwa chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ ngati chimene anthu a mitundu ina+ osadziwa Mulungu+ ali nacho.

  • 2 Atesalonika 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+

  • Chivumbulutso 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako, ndinamva mawu ofuula+ ochokera m’malo opatulika akuuza angelo 7 aja kuti: “Pitani, kathireni mbale 7 za mkwiyo+ wa Mulunguzo kudziko lapansi.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena