Yohane 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa. Aroma 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mkwiyo wa Mulungu+ ukusonyezedwa kuchokera kumwamba pa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zosalungama+ amene akupondereza choonadi+ m’njira yosalungama.+
19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa.
18 Mkwiyo wa Mulungu+ ukusonyezedwa kuchokera kumwamba pa anthu onse osaopa Mulungu ndi ochita zosalungama+ amene akupondereza choonadi+ m’njira yosalungama.+