Salimo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu oipa+ adzapita ku Manda,+Ngakhalenso anthu onse a mitundu ina amene aiwala Mulungu.+ Salimo 79:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Ndi pa maufumu amene sakuitana pa dzina lanu.+ Yesaya 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti Yehova wakwiyira mitundu yonse.+ Wapsera mtima asilikali awo onse.+ Iye awawononga ndipo awapha.+
6 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu amene akukunyalanyazani,+Ndi pa maufumu amene sakuitana pa dzina lanu.+
2 Pakuti Yehova wakwiyira mitundu yonse.+ Wapsera mtima asilikali awo onse.+ Iye awawononga ndipo awapha.+