Numeri 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma ngati angafe ndi chinthu chachilendo chimene Yehova achite,+ kuti nthaka iyasame n’kuwameza iwo+ ndi zonse ali nazo, moti iwo n’kutsikira ku Manda*+ ali amoyo, pamenepo mudziwa ndithu kuti amunawa anyoza+ Yehova.” Yesaya 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, Manda* akulitsa malo ake ndipo atsegula kwambiri pakamwa pake kupitirira malire.+ Anthu olemekezeka a mumzindawo, khamu lake, phokoso lake ndi chikondwerero chake zidzatsikira m’mandamo.+
30 Koma ngati angafe ndi chinthu chachilendo chimene Yehova achite,+ kuti nthaka iyasame n’kuwameza iwo+ ndi zonse ali nazo, moti iwo n’kutsikira ku Manda*+ ali amoyo, pamenepo mudziwa ndithu kuti amunawa anyoza+ Yehova.”
14 Choncho, Manda* akulitsa malo ake ndipo atsegula kwambiri pakamwa pake kupitirira malire.+ Anthu olemekezeka a mumzindawo, khamu lake, phokoso lake ndi chikondwerero chake zidzatsikira m’mandamo.+