Salimo 55:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chiwonongeko chiwagwere!+Atsikire ku Manda ali amoyo.+Pakuti kulikonse kumene apita, zinthu zoipa zimakhala mumtima mwawo.+ Miyambo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tiye tikawameze amoyo+ ngati mmene amachitira Manda,*+ tikawameze athunthu ngati amene akupita kudzenje.+
15 Chiwonongeko chiwagwere!+Atsikire ku Manda ali amoyo.+Pakuti kulikonse kumene apita, zinthu zoipa zimakhala mumtima mwawo.+
12 Tiye tikawameze amoyo+ ngati mmene amachitira Manda,*+ tikawameze athunthu ngati amene akupita kudzenje.+