Salimo 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kusakaza kwa mdani kwatheratu tsopano,+Mizinda imene mwaifafaniza, nayonso yatheratu.+Dzina la mdani wanu silidzatchulidwanso.+ Salimo 59:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Afafanizeni mu mkwiyo wanu.+Afafanizeni kuti asakhaleponso.Ndipo adziwe kuti Mulungu akulamulira Yakobo mpaka kumalekezero a dziko lonse lapansi.+ [Seʹlah.] Salimo 69:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Msasa wawo wokhala ndi mpanda ukhale bwinja,+Ndipo m’mahema awo musapezeke munthu wokhalamo.+ Salimo 109:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tchimo ndi cholakwacho zikhale pamaso pa Yehova nthawi zonse,+Ndipo achotse dzina lawo padziko lapansi kuti lisakumbukiridwenso,+
6 Kusakaza kwa mdani kwatheratu tsopano,+Mizinda imene mwaifafaniza, nayonso yatheratu.+Dzina la mdani wanu silidzatchulidwanso.+
13 Afafanizeni mu mkwiyo wanu.+Afafanizeni kuti asakhaleponso.Ndipo adziwe kuti Mulungu akulamulira Yakobo mpaka kumalekezero a dziko lonse lapansi.+ [Seʹlah.]
15 Tchimo ndi cholakwacho zikhale pamaso pa Yehova nthawi zonse,+Ndipo achotse dzina lawo padziko lapansi kuti lisakumbukiridwenso,+