Salimo 74:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+ Salimo 107:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa anachita zinthu mopandukira+ mawu a Mulungu,+Ndipo ananyoza malangizo a Wam’mwambamwamba.+
18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+
11 Chifukwa anachita zinthu mopandukira+ mawu a Mulungu,+Ndipo ananyoza malangizo a Wam’mwambamwamba.+