Numeri 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma ngati Yehova angawachitire chinthu chachilendo, kuti nthaka ingʼambike* nʼkuwameza ndi zonse zimene ali nazo, moti iwo nʼkutsikira ku Manda* ali amoyo, zikatero mudziwa ndithu kuti amunawa anyoza Yehova.”
30 Koma ngati Yehova angawachitire chinthu chachilendo, kuti nthaka ingʼambike* nʼkuwameza ndi zonse zimene ali nazo, moti iwo nʼkutsikira ku Manda* ali amoyo, zikatero mudziwa ndithu kuti amunawa anyoza Yehova.”