Numeri 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma ngati angafe ndi chinthu chachilendo chimene Yehova achite,+ kuti nthaka iyasame n’kuwameza iwo+ ndi zonse ali nazo, moti iwo n’kutsikira ku Manda*+ ali amoyo, pamenepo mudziwa ndithu kuti amunawa anyoza+ Yehova.”
30 Koma ngati angafe ndi chinthu chachilendo chimene Yehova achite,+ kuti nthaka iyasame n’kuwameza iwo+ ndi zonse ali nazo, moti iwo n’kutsikira ku Manda*+ ali amoyo, pamenepo mudziwa ndithu kuti amunawa anyoza+ Yehova.”