Salimo 50:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+ Yesaya 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti Yehova wakwiyira mitundu yonse.+ Wapsera mtima asilikali awo onse.+ Iye awawononga ndipo awapha.+ Yeremiya 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu+ amene akunyalanyazani,+ ndi pa mafuko amene sakuitana padzina lanu.+ Pakuti iwo adya Yakobo.+ Amudya ndipo akupitirizabe kumuwononga.+ Malo ake okhalamo awasandutsa bwinja.+
22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+
2 Pakuti Yehova wakwiyira mitundu yonse.+ Wapsera mtima asilikali awo onse.+ Iye awawononga ndipo awapha.+
25 Tsanulirani mkwiyo wanu pa mitundu ya anthu+ amene akunyalanyazani,+ ndi pa mafuko amene sakuitana padzina lanu.+ Pakuti iwo adya Yakobo.+ Amudya ndipo akupitirizabe kumuwononga.+ Malo ake okhalamo awasandutsa bwinja.+