Salimo 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+ Salimo 140:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+ Miyambo 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pali m’badwo umene mano ake ali ngati malupanga ndiponso umene nsagwada zake zili ngati mipeni yophera nyama,+ kuti m’badwowo udye osautsidwa onse a padziko lapansi ndiponso anthu osauka pakati pa anthu.+
14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+
12 Ndikudziwa bwino kwambiri kuti Yehova adzazengera+Mlandu anthu osautsika. Iye adzachitira chilungamo anthu osauka.+
14 Pali m’badwo umene mano ake ali ngati malupanga ndiponso umene nsagwada zake zili ngati mipeni yophera nyama,+ kuti m’badwowo udye osautsidwa onse a padziko lapansi ndiponso anthu osauka pakati pa anthu.+