Yesaya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi amuna inu mukutanthauza chiyani pophwanya anthu anga ndi kupera nkhope za anthu ovutika?”+ akutero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.
15 Kodi amuna inu mukutanthauza chiyani pophwanya anthu anga ndi kupera nkhope za anthu ovutika?”+ akutero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.