Yesaya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nʼchifukwa chiyani mukuphwanya anthu angaKomanso kukhulitsa nkhope za anthu osauka padothi?”+ akutero Ambuye Wamkulu Koposa, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Yesaya 1, tsa. 58
15 Nʼchifukwa chiyani mukuphwanya anthu angaKomanso kukhulitsa nkhope za anthu osauka padothi?”+ akutero Ambuye Wamkulu Koposa, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.