Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 58:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndithu inuyo munali kusala kudya n’cholinga choti muzikangana, kulimbana,+ ndiponso kuti muzimenyana ndi nkhonya zovulaza.+ Kodi inuyo simunali kusala kudya n’kumaganiza kuti inali nthawi yoti mawu anu amveke kumwamba?

  • Amosi 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Yehova wanena kuti, ‘Popeza kuti Isiraeli anapanduka mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anagulitsa munthu wolungama kuti apeze siliva komanso anagulitsa munthu wosauka pa mtengo wa nsapato.+

  • Amosi 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Tamverani izi amuna inu, inu amene mukufuna kumeza munthu wosauka+ ndiponso amene mukufuna kufafaniza anthu ofatsa padziko lapansi.+

  • Mika 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Inu mumadana ndi zinthu zabwino+ ndi kukonda zinthu zoipa.+ Mumasenda khungu la anthu ndi kuchotsa mnofu pamafupa awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena