Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 22:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Poyankha, mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati kuti: “Pali munthu mmodzi amene tingathe kufunsira kwa Yehova kudzera mwa iye,+ koma ineyo ndimadana naye kwambiri,+ chifukwa salosera zabwino zokhudza ine, koma zoipa.+ Munthuyo dzina lake ndi Mikaya mwana wa Imula.” Koma Yehosafati anati: “Musalankhule choncho mfumu.”+

  • Amosi 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Anthuwo amadana ndi munthu wowadzudzula pachipata cha mzinda,+ komanso amanyansidwa ndi munthu wowauza chilungamo.+

  • Luka 19:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma nzika zinzake zinadana naye+ ndipo m’mbuyo muno zinatumiza akazembe kuti apite akanene kuti, ‘Ife sitikufuna kuti munthu uyu akhale mfumu yathu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena