1 Mafumu 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+ Miyambo 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zimene umakhumba zikapezeka, moyo umasangalala.+ Koma opusa, kusiya zoipa kumawanyansa.+ Yesaya 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 amene amachimwitsa munthu ndi mawu ake,+ amene amatchera msampha munthu wodzudzula ena pachipata,+ ndiponso amene amagwiritsira ntchito mfundo zopanda umboni pokankhira pambali munthu wolungama.+
17 Ahabu atangomuona Eliya, anati: “Ndiwe eti! Iwe ndiwe munthu amene wachititsa kuti Isiraeli anyanyalidwe.”+
21 amene amachimwitsa munthu ndi mawu ake,+ amene amatchera msampha munthu wodzudzula ena pachipata,+ ndiponso amene amagwiritsira ntchito mfundo zopanda umboni pokankhira pambali munthu wolungama.+