1 Mafumu 1:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Komanso mfumu inati, ‘Adalitsike+ Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene lero wapereka munthu woti akhale pampando wanga wachifumu, ine ndikuona ndi maso anga.’”+
48 Komanso mfumu inati, ‘Adalitsike+ Yehova Mulungu wa Isiraeli, amene lero wapereka munthu woti akhale pampando wanga wachifumu, ine ndikuona ndi maso anga.’”+