Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja. 2 Mafumu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero Yehova anawakwiyira kwambiri+ Aisiraeli ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.+ Salimo 78:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+ Amosi 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti ndidzakupititsani ku ukapolo, kutali kwambiri ndi ku Damasiko,’+ watero Mulungu wa makamu, amene dzina lake ndi Yehova.”+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja.
18 Chotero Yehova anawakwiyira kwambiri+ Aisiraeli ndipo anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.+
60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+
27 Pakuti ndidzakupititsani ku ukapolo, kutali kwambiri ndi ku Damasiko,’+ watero Mulungu wa makamu, amene dzina lake ndi Yehova.”+