Salimo 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwatipereka kwa adani athu kuti atidye ngati nkhosa,+Ndipo mwatimwaza pakati pa anthu a mitundu ina.+ Yeremiya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzawamwaza pakati pa mitundu ya anthu imene iwo kapena makolo awo sanaidziwe.+ Ndidzawakantha ndi lupanga kufikira nditawafafaniza.’+
11 Mwatipereka kwa adani athu kuti atidye ngati nkhosa,+Ndipo mwatimwaza pakati pa anthu a mitundu ina.+
16 Ndidzawamwaza pakati pa mitundu ya anthu imene iwo kapena makolo awo sanaidziwe.+ Ndidzawakantha ndi lupanga kufikira nditawafafaniza.’+