Salimo 119:176 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 176 Ndayendayenda ngati nkhosa yosochera.+ Ndifunefuneni ine mtumiki wanu,+Pakuti sindinaiwale malamulo anu.+ Aroma 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+
176 Ndayendayenda ngati nkhosa yosochera.+ Ndifunefuneni ine mtumiki wanu,+Pakuti sindinaiwale malamulo anu.+
36 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Chifukwa cha inu, tikuphedwa nthawi zonse. Takhala ngati nkhosa zokaphedwa.”+