Levitiko 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Amenewa ndiwo malamulo+ amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa ana a Isiraeli. Salimo 119:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Ndinafulumira ndipo sindinazengereze+Kusunga malamulo anu.+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita. Hoseya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+
34 Amenewa ndiwo malamulo+ amene Yehova anapatsa Mose paphiri la Sinai+ kuti apereke kwa ana a Isiraeli.
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+