Levitiko 26:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Amenewa ndiwo malangizo, zigamulo+ ndi malamulo amene Yehova anaika pakati pa iye ndi ana a Isiraeli m’phiri la Sinai, kudzera mwa Mose.+ Deuteronomo 4:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Chilamulocho ndicho maumboni,*+ malangizo+ ndi zigamulo+ zimene Mose anauza ana a Isiraeli pamene anatuluka mu Iguputo.
46 Amenewa ndiwo malangizo, zigamulo+ ndi malamulo amene Yehova anaika pakati pa iye ndi ana a Isiraeli m’phiri la Sinai, kudzera mwa Mose.+
45 Chilamulocho ndicho maumboni,*+ malangizo+ ndi zigamulo+ zimene Mose anauza ana a Isiraeli pamene anatuluka mu Iguputo.